Yohane 9:36 - Buku Lopatulika36 Iyeyu anayankha nati, Ndipo ndani Iye, Ambuye, kuti ndimkhulupirire Iye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Iyeyu anayankha nati, Ndipo ndani Iye, Ambuye, kuti ndimkhulupirire Iye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Iye adati, “Ambuye, mundiwuzetu ndani Iyeyo, kuti ndimkhulupirire.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Munthuyo anafunsa kuti, “Kodi, Ambuye, ameneyo ndi ndani? Ndiwuzeni kuti ndimukhulupirire Iye?” Onani mutuwo |