Yohane 9:19 - Buku Lopatulika19 nawafunsa iwo, nanena, Kodi uyu ndi mwana wanu, amene inu munena kuti anabadwa wosaona? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 nawafunsa iwo, nanena, Kodi uyu ndi mwana wanu, amene inu munena kuti anabadwa wosaona? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono adaŵafunsa kuti, “Kodi inu, uyu ndi mwana wanu? Ndiye mukuti adaabadwadi wosapenya? Nanga zatani kuti tsopano akupenya?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Iwo anafunsa kuti, “Kodi uyu ndi mwana wanu? Kodi iyeyu ndi amene mukunena kuti anabadwa wosaona? Nanga zikutheka bwanji kuti akuona?” Onani mutuwo |