Yohane 9:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo apenya bwanji tsopano? Atate wake ndi amake anayankha nati, Tidziwa kuti uyu ndi mwana wathu, ndi kuti anabadwa wosaona; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo apenya bwanji tsopano? Atate wake ndi amake anayankha nati, Tidziwa kuti uyu ndi mwana wathu, ndi kuti anabadwa wosaona; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Makolo ake adati, “Chimene tikudziŵa ife nchakuti ameneyu ndi mwana wathu, ndipo adaabadwadi wosapenya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Makolo anayankha kuti, “Ife tikudziwa kuti ndi mwana wathu, ndipo tikudziwa kuti anabadwa wosaona. Onani mutuwo |