Yohane 9:18 - Buku Lopatulika18 Chifukwa chake Ayuda sanakhulupirire za iye, kuti anali wosaona, napenya, kufikira kumene adaitana atate wake ndi amake a iye wopenya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Chifukwa chake Ayuda sanakhulupirire za iye, kuti anali wosaona, napenya, kufikira kumene adaitana atate wake ndi amake a iye wopenya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Koma akulu a Ayudawo sadakhulupirire kuti munthuyo kale sankapenya ndipo tsopano akupenya, mpaka adaitanitsa makolo ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ayuda sanakhulupirirebe kuti iye anali wosaona ndi kuti anayamba kuona kufikira atayitana makolo ake. Onani mutuwo |