Yohane 9:13 - Buku Lopatulika13 Anapita naye amene anali wosaona kale kwa Afarisi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Anapita naye amene anali wosaona kale kwa Afarisi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono munthu uja kale sankapenyayu adapita naye kwa Afarisi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iwo anabwera naye munthu amene poyamba anali wosaona kwa Afarisi. Onani mutuwo |