Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 9:14 - Buku Lopatulika

14 Koma tsikulo ndi la Sabata limene Yesu anakanda thope, namtsegulira iye maso ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Koma tsikulo ndi la Sabata limene Yesu anakanda thope, namtsegulira iye maso ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Tsiku limene Yesu adaakanda thope namchiritsalo linali la Sabata.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Tsono linali la Sabata tsiku limene Yesu anakanda dothi ndi kutsekula maso a munthuyu.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 9:14
11 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali kuti anapita Iye pakati pa minda tsiku la Sabata; ndipo ophunzira ake poyenda anayamba kubudula ngala za dzinthu.


Ndipo panali pamene Iye analowa m'nyumba ya mmodzi wa akulu a Afarisi tsiku la Sabata, kukadya, iwo analikumzonda Iye.


Ndipo chifukwa cha ichi Ayuda analondalonda Yesu, popeza anachita izo tsiku la Sabata.


Ndipo pomwepo munthuyu anachira, nayalula mphasa yake, nayenda. Koma tsiku lomwelo linali la Sabata.


Anapita naye amene anali wosaona kale kwa Afarisi.


Pamene ananena izi, analavula pansi, nakanda thope ndi malovuwo, napaka thopelo m'maso,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa