Yohane 9:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anati kwa iye, Ali kuti Iyeyo? Anena, Sindidziwa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anati kwa iye, Ali kuti Iyeyo? Anena, Sindidziwa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Anthuwo adamufunsa kuti, “Iyeyo ali kuti?” Munthu uja adati, “Kaya, sindikudziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iwo anamufunsa iye kuti, “Ali kuti munthu ameneyu?” Iye anati, “Ine sindikudziwa.” Onani mutuwo |