Yohane 8:9 - Buku Lopatulika9 Koma iwo, m'mene anatulukamo amodziamodzi, kuyambira akulu, kufikira otsiriza; ndipo Yesu anatsala yekha, ndi mkazi, alikuima pakati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma iwo, m'mene anatulukamo amodziamodzi, kuyambira akulu, kufikira otsiriza; ndipo Yesu anatsala yekha, ndi mkazi, alikuima pakati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma iwo atamva zimenezi, adayamba kuchokapo mmodzimmodzi, kuyambira akuluakulu; Yesu nkutsalira yekha, mai uja ali chikhalire pakati pompaja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Iwo atamva izi anayamba kuchoka mmodzimmodzi, akuluakulu poyamba, mpaka Yesu anatsala yekha ndi mkaziyo atayimirira pomwepo. Onani mutuwo |