Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 8:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo m'mene adaweramanso analemba ndi chala chake pansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo m'mene adaweramanso analemba ndi chala chake pansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Atatero, adaŵeramanso namalemba pansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Iye anaweramanso pansi ndi kulemba pa dothi.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 8:8
3 Mawu Ofanana  

natenge madzi opatulika m'mbale yadothi wansembeyo, natengeko fumbi lili pansi mu chihema, wansembeyo nalithire m'madzimo.


Koma pamene anakhalakhala alikumfunsabe Iye, anaweramuka, nati kwa iwo, Amene mwa inu ali wopanda tchimo, ayambe kumponya mwala.


Koma iwo, m'mene anatulukamo amodziamodzi, kuyambira akulu, kufikira otsiriza; ndipo Yesu anatsala yekha, ndi mkazi, alikuima pakati.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa