Yohane 8:57 - Buku Lopatulika57 Ayuda pamenepo anati kwa Iye, Simunafikire zaka makumi asanu, ndipo munaona Abrahamu kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201457 Ayuda pamenepo anati kwa Iye, Simunafikire zaka makumi asanu, ndipo munaona Abrahamu kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa57 Apo Ayuda adamufunsa kuti, “Zaka zako sizinakwane ndi makumi asanu omwe, ndiye nkukhala utaona Abrahamu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero57 Ayuda anati kwa Iye, “Inu sumunafike nʼkomwe zaka makumi asanu, ndipo mukuti munamuona Abrahamu!” Onani mutuwo |