Yohane 8:49 - Buku Lopatulika49 Yesu anayankha, Ndilibe chiwanda Ine; koma ndilemekeza Atate wanga, ndipo inu mundipeputsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Yesu anayankha, Ndilibe chiwanda Ine; koma ndilemekeza Atate wanga, ndipo inu mundipeputsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Yesu adati, “Ine sindidagwidwe ndi mizimu yoipa. Ndimalemekeza Atate anga, koma inu mumandipeputsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Yesu anati, “Ine sindinagwidwe ndi chiwanda, koma ndimalemekeza Atate anga, koma inu mukundinyoza. Onani mutuwo |