Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 8:50 - Buku Lopatulika

50 Koma Ine sinditsata ulemerero wanga; alipo woutsata ndi wakuweruza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

50 Koma Ine sinditsata ulemerero wanga; alipo woutsata ndi wakuweruza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

50 Komabe Ine sindidzifunira ndekha ulemu. Alipo wina wondifunira ulemu, ndiye amaweruza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

50 Ine sindidzifunira ndekha ulemu; koma alipo wina amene amandifunira, ndipo Iyeyo ndiye woweruza.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 8:50
6 Mawu Ofanana  

Ulemu sindiulandira kwa anthu.


Musayesa kuti Ine ndidzakunenezani inu kwa Atate; pali wakukunenezani, ndiye Mose, amene inu mumtama.


Iye wolankhula zochokera kwa iye yekha afuna ulemu wa mwini yekha. Iye wakufuna ulemu wa Iye amene anamtuma, yemweyu ali woona, ndipo mwa Iye mulibe chosalungama.


Yesu anayankha, Ngati Ine ndidzilemekeza ndekha, ulemerero wanga uli chabe; Atate wanga ndiye wondilemekeza Ine; amene munena za Iye, kuti ndiye Mulungu wanu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa