Yohane 8:43 - Buku Lopatulika43 Simuzindikira malankhulidwe anga chifukwa ninji? Chifukwa simungathe kumva mau anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Simuzindikira malankhulidwe anga chifukwa ninji? Chifukwa simungathe kumva mau anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Nanga chifukwa chiyani simukumvetsa zimene ndikunena? Chifukwa chake nchakuti simungakonde konse kumva mau anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Nʼchifukwa chiyani simukumvetsetsa mawu anga? Chifukwa chake nʼchakuti simungathe kumva zoyankhula zanga. Onani mutuwo |