Yohane 8:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo ngati ndiweruza Ine, chiweruziro changa chili choona; pakuti sindili pa ndekha, koma Ine ndi Atate amene anandituma Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo ngati ndiweruza Ine, chiweruziro changa chili choona; pakuti sindili pa ndekha, koma Ine ndi Atate amene anandituma Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma ndikati ndiweruze, ndimaweruza molungama, pakuti sindili ndekha ai, palinso Atate amene adandituma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma Ine ndikati ndiweruze, ndimaweruza molondola, chifukwa Ine sindili ndekha koma ndili ndi Atate amene anandituma. Onani mutuwo |