Yohane 8:15 - Buku Lopatulika15 Inu muweruza monga mwa thupi; Ine sindiweruza munthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Inu muweruza monga mwa thupi; Ine sindiweruza munthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Inu mumaweruza potsata maganizo a anthu chabe. Ine sindiweruza munthu aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Inu mumaweruza potsata maganizo a anthu chabe. Ine sindiweruza munthu wina aliyense. Onani mutuwo |