Yohane 7:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo m'mene adanena nao zimenezi anakhalabe mu Galileya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo m'mene adanena nao zimenezi anakhalabe m'Galileya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Yesu atanena zimenezo, adatsalira m'Galileya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Atanena izi, Iye anakhalabe mu Galileya. Onani mutuwo |