Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 7:8 - Buku Lopatulika

8 Kwerani inu kunka kuphwando; sindikwera Ine kuphwando ili tsopano apa; pakuti nthawi yanga siinakwanire.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Kwerani inu kunka kuphwando; sindikwera Ine kuphwando ili tsopano apa; pakuti nthawi yanga siinakwanire.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Inuyo pitani kuchikondwereroko. Ine sindipitako ku chikondwerero chimenechi, chifukwa nthaŵi yanga yoyenera siinafike.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Inu pitani kuphwando. Ine sindipita tsopano kuphwando ili chifukwa kwa Ine nthawi yoyenera sinafike.”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 7:8
9 Mawu Ofanana  

Nati Iye, Mukani kumzinda kwa munthu wina wake, mukati kwa Iye, Mphunzitsi anena, Nthawi yanga yayandikira; ndidzadya Paska kwanu pamodzi ndi ophunzira anga.


Yesu nanena naye, Mkazi, ndili ndi chiyani ndi inu? Nthawi yanga siinafike.


Pamenepo anafuna kumgwira Iye; koma palibe wina anamgwira kumanja, chifukwa nthawi yake siinafike.


Chifukwa chake Yesu ananena nao, Nthawi yanga siinafike; koma nthawi yanu yakonzeka masiku onse.


Ndipo m'mene adanena nao zimenezi anakhalabe mu Galileya.


Mau awa analankhula m'nyumba yosungiramo chuma cha Mulungu pophunzitsa mu Kachisi; ndipo palibe munthu anamgwira Iye, pakuti nthawi yake siinafike.


Pakulankhula Iye zimenezi ambiri anakhulupirira Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa