Yohane 7:10 - Buku Lopatulika10 Koma pamene abale ake adakwera kunka kuchikondwerero, pomwepo Iyenso anakwera, si poonekera, koma monga mobisalika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma pamene abale ake adakwera kunka kuchikondwerero, pomwepo Iyenso anakwera, si poonekera, koma monga mobisalika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Koma abale ake atapita ku chikondwerero cha Misasa chija, Yesu nayenso adapitako. Sadapite moonekera, koma mobisika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Komabe, abale ake atanyamuka kupita kuphwando, Iye anapitanso, osati moonekera, koma mseri. Onani mutuwo |