Yohane 7:11 - Buku Lopatulika11 Pomwepo Ayuda analikumfuna Iye pachikondwerero, nanena, Ali kuti uja? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pomwepo Ayuda analikumfuna Iye pachikondwerero, nanena, Ali kuti uja? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Akulu a Ayuda ankamufunafuna kuchikondwereroko, nkumafunsana kuti, “Kodi amene uja ali kuti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsopano kuphwandoko Ayuda anakamufunafuna ndi kumafunsana kuti, “Kodi munthu ameneyu ali kuti?” Onani mutuwo |