Yohane 7:46 - Buku Lopatulika46 Anyamatawo anayankha, Nthawi yonse palibe munthu analankhula chotero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201446 Anyamatawo anayankha, Nthawi yonse palibe munthu analankhula chotero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa46 Asilikali aja adayankha kuti, “Palibenso wina amene adalankhulapo ngati munthu ameneyo nkale lonse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero46 Asilikali aja anati, “Palibe wina amene anayankhula ngati Munthu ameneyo nʼkale lonse.” Onani mutuwo |