Yohane 7:45 - Buku Lopatulika45 Pamenepo anyamatawo anadza kwa ansembe aakulu ndi Afarisi; ndipo iwowa anati kwa iwo, Simunamtenge Iye bwanji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Pamenepo anyamatawo anadza kwa ansembe aakulu ndi Afarisi; ndipo iwowa anati kwa iwo, Simunamtenga Iye bwanji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Asilikali a ku Nyumba ya Mulungu aja adabwerera kwa akulu a ansembe ndi kwa Afarisi aja. Iwo adafunsa asilikaliwo kuti, “Bwanji simudabwere naye?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Pomaliza asilikali a mʼNyumba ya Mulungu anabwerera kwa akulu a ansembe ndi Afarisi amene anawafunsa iwo kuti, “Kodi ndi chifukwa chiyani simunamugwire Iye?” Onani mutuwo |