Yohane 7:44 - Buku Lopatulika44 Koma ena mwa iwo anafuna kumgwira Iye; koma palibe munthu anamgwira kumanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Koma ena mwa iwo anafuna kumgwira Iye; koma palibe munthu anamgwira kumanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Ena ankafuna kumgwira, koma panalibe amene adamkhudza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Ena anafuna kumugwira Iye, koma palibe amene anayika dzanja pa Iye. Onani mutuwo |