Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 7:43 - Buku Lopatulika

43 Kudakhala tsono kusiyana m'khamulo chifukwa cha Iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 Kudakhala tsono kusiyana m'khamulo chifukwa cha Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

43 Choncho khamu la anthu lidagaŵikana chifukwa cha Iye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Kotero anthu anagawikana chifukwa cha Yesu.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 7:43
7 Mawu Ofanana  

Pakuti ndinadza kusiyanitsa munthu ndi atate wake, ndi mwana wamkazi ndi amake, ndi mkazi wokwatiwa ndi mpongozi wake:


Kodi muyesa kuti ndinadzera kudzapatsa mtendere padziko lapansi? Ndinena kwa inu, Iaitu, komatu kutsutsana;


Panakhalanso kutsutsana pakati pa Ayuda chifukwa cha mau awa.


Ndipo kunali kung'ung'udza kwambiri za Iye m'makamu a anthu; ena ananena, kuti, Ali wabwino; koma ena ananena, Iai, koma asocheretsa khamu la anthuwo.


Ena pamenepo mwa Afarisi ananena, Munthu uyu sachokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata. Koma ena ananena, Munthu ali wochimwa akhoza bwanji kuchita zizindikiro zotere? Ndipo panali kutsutsana mwa iwo.


Ndipo khamu la mzindawo linagawikana; ena anali ndi Ayuda, koma ena anali ndi atumwi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa