Yohane 7:34 - Buku Lopatulika34 Mudzafunafuna Ine, osandipeza; ndipo pomwe ndili Ine, inu simungathe kudzapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Mudzafunafuna Ine, osandipeza; ndipo pomwe ndili Ine, inu simungathe kudzapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Mudzandifunafuna, koma simudzandipeza. Ndipo kumene ndizikakhala Ine, inu simungathe kufikako.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Inu mudzandifunafuna koma simudzandipeza; ndipo kumene Ine ndili inu simungathe kubwera.” Onani mutuwo |