Yohane 7:25 - Buku Lopatulika25 Pamenepo ena a iwo a ku Yerusalemu ananena, Kodi suyu amene afuna kumupha? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pamenepo ena a iwo a ku Yerusalemu ananena, Kodi suyu amene afuna kumupha? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pamenepo anthu ena a ku Yerusalemu adati, “Kodi munthu akufuna kumupha uja, si ameneyu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pa nthawi imeneyi anthu ena a ku Yerusalemu anayamba kufunsana kuti, “Kodi uyu si munthu uja akufuna kumuphayu? Onani mutuwo |