Yohane 7:24 - Buku Lopatulika24 Musaweruze monga maonekedwe, koma weruzani chiweruziro cholungama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Musaweruze monga maonekedwe, koma weruzani chiweruziro cholungama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Musamaweruza poyang'ana maonekedwe chabe, koma muziweruza molungama.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Musamaweruze potengera maonekedwe chabe, koma weruzani molungama.” Onani mutuwo |