Yohane 7:22 - Buku Lopatulika22 Chifukwa cha ichi Mose anakupatsani inu mdulidwe (si kuti uchokera kwa Mose, koma kwa makolo); ndipo mudula munthu tsiku la Sabata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Chifukwa cha ichi Mose anakupatsani inu mdulidwe (si kuti uchokera kwa Mose, koma kwa makolo); ndipo mudula munthu tsiku la Sabata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Mose adakulamulani kuti muziwumbala ana anu aamuna (ngakhale mwambowo si wochokera kwa Mose koma kwa makolo); ndipo inu mumaumbala mwana wamwamuna ngakhale mpa tsiku la Sabata. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Koma, chifukwa chakuti Mose anakulamulani kuti muzichita mdulidwe (ngakhale kuti sunachokere kwa Mose, koma kwa makolo anu), inuyo mumachita mdulidwe mwana tsiku la Sabata. Onani mutuwo |