Yohane 7:21 - Buku Lopatulika21 Yesu anayankha nati kwa iwo, Ndinachita ntchito imodzi, ndipo muzizwa monse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Yesu anayankha nati kwa iwo, Ndinachita ntchito imodzi, ndipo muzizwa monse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Yesu adati, “Ndinangochita ntchito yozizwitsa imodzi yokha, nonsenu nkumadabwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Yesu anawawuza kuti, “Ine ndinachita chodabwitsa chimodzi ndipo inu mwadabwa. Onani mutuwo |