Yohane 6:8 - Buku Lopatulika8 Mmodzi wa ophunzira ake, Andrea, mbale wake wa Simoni Petro, ananena ndi Iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mmodzi wa ophunzira ake, Andrea, mbale wake wa Simoni Petro, ananena ndi Iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Wophunzira wake wina, dzina lake Andrea, mbale wake wa Simoni Petro, adauza Yesu kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mmodzi wa ophunzira ake, Andreya, mʼbale wa Simoni Petro, anati, Onani mutuwo |