Yohane 6:60 - Buku Lopatulika60 Pamenepo ambiri a ophunzira ake, pakumva izi, anati, Mau awa ndi osautsa; akhoza kumva awa ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201460 Pamenepo ambiri a ophunzira ake, pakumva izi, anati, Mau awa ndi osautsa; akhoza kumva awa ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa60 Ophunzira ambiri a Yesu atamva zimenezi adati, “Mau ameneŵa ngapatali. Angathe kuŵavomera ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero60 Pakumva izi ambiri a ophunzira ake anati, “Ichi ndi chiphunzitso chovuta. Angachilandire ndani?” Onani mutuwo |