Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 6:59 - Buku Lopatulika

59 Izi ananena m'sunagoge, pakuphunzitsa mu Kapernao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

59 Izi ananena m'sunagoge, pakuphunzitsa m'Kapernao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

59 Yesu adanena zimenezi pamene ankaphunzitsa m'nyumba yamapemphero ya ku Kapernao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

59 Iye ankanena izi pamene ankaphunzitsa mʼsunagoge mu Kaperenawo.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 6:59
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Yesu anayendayenda mu Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira Uthenga Wabwino wa Ufumu, nachiritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.


Ndipo Iye anatsika nadza ku Kapernao, ndiwo mzinda wa ku Galileya. Ndipo analikuwaphunzitsa iwo pa Sabata; ndipo anadabwa ndi chiphunzitso chake;


Yesu anayankha iye, Ine ndalankhula zomveka kwa dziko lapansi; ndinaphunzitsa Ine nthawi zonse m'sunagoge ndi mu Kachisi, kumene amasonkhana Ayuda onse; ndipo mobisika sindinalankhule kanthu.


ndipo pamene adalowa m'ngalawa, analikuoloka nyanja kunka ku Kapernao. Ndipo kutada pamenepo, koma Yesu asanadze kwa iwo.


chifukwa chake pamene khamu la anthu linaona kuti palibe Yesu, ndi ophunzira ake palibe, iwo okha analowa m'ngalawazo nadza ku Kapernao, alikufuna Yesu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa