Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 6:17 - Buku Lopatulika

17 ndipo pamene adalowa m'ngalawa, analikuoloka nyanja kunka ku Kapernao. Ndipo kutada pamenepo, koma Yesu asanadze kwa iwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 ndipo pamene adalowa m'ngalawa, analikuoloka nyanja kunka ku Kapernao. Ndipo kutada pamenepo, koma Yesu asanadze kwa iwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Kumeneko adaloŵa m'chombo, nayamba kuwoloka nyanja kupita ku Kapernao. Mdima udagwa, Yesu osafikabe kwa iwo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 kumene iwo analowa mʼbwato ndi kuyamba kuwoloka nyanja kupita ku Kaperenawo. Tsopano kunali kutada ndipo Yesu anali asanabwerere kwa iwo.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 6:17
6 Mawu Ofanana  

Ndipo pomwepo Iye anakakamiza ophunzira ake alowe m'ngalawa, ndi kumtsogolera kutsidya lija ku Betsaida, m'mene Iye yekha alimkuuza khamulo kuti amuke.


Zitapita izi anatsikira ku Kapernao, Iye ndi amake, ndi abale ake, ndi ophunzira ake; nakhala komweko masiku owerengeka.


Chifukwa chake Yesu anadzanso ku Kana wa mu Galileya, kumene anasandutsa madzi vinyo. Ndipo kunali mkulu wina wa mfumu, mwana wake anadwala mu Kapernao.


Ndipo nyanja inalikuuka chifukwa cha mphepo yaikulu yakuombako.


Izi ananena m'sunagoge, pakuphunzitsa mu Kapernao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa