Yohane 6:16 - Buku Lopatulika16 Koma pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira kunyanja; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira kunyanja; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 M'mene kunkayamba kuda, ophunzira ake a Yesu adatsikira ku nyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira ku nyanja, Onani mutuwo |