Yohane 6:1 - Buku Lopatulika1 Zitapita izi anachoka Yesu kunka kutsidya lija la nyanja ya Galileya, ndiyo ya Tiberiasi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Zitapita izi anachoka Yesu kunka kutsidya lija la nyanja ya Galileya, ndiyo ya Tiberiasi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Yesu adaoloka nyanja ya Galileya (dzina lake lina ndi nyanja ya Tiberiasi.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Nthawi ina zitatha izi, Yesu anawolokera ku gombe la kutali la nyanja ya Galileya (iyi ndi nyanja ya Tiberiya), Onani mutuwo |