Yohane 5:47 - Buku Lopatulika47 Koma ngati simukhulupirira malembo a iyeyu, mudzakhulupirira bwanji mau anga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Koma ngati simukhulupirira malembo a iyeyu, mudzakhulupirira bwanji mau anga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Koma ngati simukhulupirira zimene iyeyo adalemba, nanga mungakhulupirire bwanji mau anga?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Koma ngati simukhulupirira zimene iye analemba, mudzakhulupirira bwanji zimene Ine ndikunena?” Onani mutuwo |