Yohane 5:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo chifukwa cha ichi Ayuda analondalonda Yesu, popeza anachita izo tsiku la Sabata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo chifukwa cha ichi Ayuda analondalonda Yesu, popeza anachita izo tsiku la Sabata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Popeza kuti linali tsiku la Sabata pamene Yesu adaachita zimenezi, Ayuda adayamba kumuvutitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo popeza Yesu amachita zinthu izi tsiku la Sabata, Ayuda anayamba kumulondalonda. Onani mutuwo |