Yohane 5:13 - Buku Lopatulika13 Koma wochiritsidwayo sanadziwe kuti anali ndani; pakuti Yesu anachoka kachetechete, popeza panali anthu aunyinji m'malo muja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma wochiritsidwayo sanadziwe kuti anali ndani; pakuti Yesu anachoka kachetechete, popeza panali anthu aunyinji m'malo muja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Koma wochirayo sadamdziŵe, popeza kuti Yesu anali ataloŵerera m'kati mwa anthu ambiri amene anali pamenepo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Munthu amene anachiritsidwayo sanadziwe kuti anali ndani, pakuti Yesu anangolowera mʼgulu la anthu ndi kupita. Onani mutuwo |