Yohane 5:12 - Buku Lopatulika12 Anamfunsa, Munthuyo ndani wonena ndi iwe, Yalula mphasa yako, nuyende? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Anamfunsa, Munthuyo ndani wonena ndi iwe, Yalula mphasa yako, nuyende? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Iwo adamufunsa kuti, “Munthuyo ndani amene wakuuza kuti unyamule mphasa yako, uyende?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamenepo anamufunsa iye kuti, “Kodi munthu ameneyo ndani amene wakuwuza kuti, ‘Nyamula mphasa yako ndipo yenda?’ ” Onani mutuwo |