Yohane 5:11 - Buku Lopatulika11 Koma iyeyu anayankha iwo, Iye amene anandichiritsa, yemweyu anati kwa ine, Yalula mphasa yako, nuyende. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma iyeyu anayankha iwo, Iye amene anandichiritsa, yemweyu anati kwa ine, Yalula mphasa yako, nuyende. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma iye adati, “Amene wandichiritsa ndiye wandiwuza kuti, ‘Nyamula mphasa yako, yenda.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma iye anayankha kuti, “Munthu amene wandichiritsa anati kwa ine, ‘Nyamula mphasa yako yamba kuyenda.’ ” Onani mutuwo |