Yohane 5:1 - Buku Lopatulika1 Zitapita izi panali chikondwerero cha Ayuda; ndipo Yesu anakwera kunka ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Zitapita izi panali chikondwerero cha Ayuda; ndipo Yesu anakwera kunka ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake kunali chikondwerero chachipembedzo cha Ayuda, ndipo Yesu adapitako ku Yerusalemuko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patapita nthawi Yesu anakwera kupita ku Yerusalemu ku phwando la Ayuda. Onani mutuwo |