Yohane 4:54 - Buku Lopatulika54 Ichi ndi chizindikiro chachiwiri Yesu anachita, atachokera ku Yudeya, ndi kulowa mu Galileya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201454 Ichi ndi chizindikiro chachiwiri Yesu anachita, atachokera ku Yudeya, ndi kulowa m'Galileya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa54 Ichi chinali chizindikiro chachiŵiri chimene Yesu adaonetsa atafika ku Galileya kuchokera ku Yudeya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero54 Ichi ndiye chinali chizindikiro chodabwitsa chachiwiri chimene Yesu anachita atafika ku Galileya kuchokera ku Yudeya. Onani mutuwo |