Yohane 4:44 - Buku Lopatulika44 Pakuti Yesu mwini anachita umboni kuti, Mneneri alibe ulemu m'dziko la kwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Pakuti Yesu mwini anachita umboni kuti, Mneneri alibe ulemu m'dziko la kwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Mwiniwakeyo anali atanena kuti, “Mneneri, anthu akwao samchitira ulemu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 (Tsopano Yesu mwini ananena kale kuti mneneri salandira ulemu mʼdziko lake). Onani mutuwo |