Yohane 4:40 - Buku Lopatulika40 Chifukwa chake pamene Asamariya anadza kwa Iye, anamfunsa akhale nao; ndipo anakhala komweko masiku awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Chifukwa chake pamene Asamariya anadza kwa Iye, anamfunsa akhale nao; ndipo anakhala komweko masiku awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Tsono pamene Asamariyawo adafika kwa Yesu, adampempha kuti akhale nao kwaoko. Ndipo adakhaladi komweko masiku aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Choncho Asamariya atabwera kwa Iye, anamuwumiriza Iye kuti akhale nawo, ndipo Iye anakhala nawo masiku awiri. Onani mutuwo |