Yohane 4:36 - Buku Lopatulika36 Wakumweta alandira kulipira, nasonkhanitsira chobala kumoyo wosatha; kuti wofesayo akakondwere pamodzi ndi womwetayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Wakumweta alandira kulipira, nasonkhanitsira chobala kumoyo wosatha; kuti wofesayo akakondwere pamodzi ndi womwetayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Okolola ayamba kale kulandira malipiro, ndipo akututira mbeu ku moyo wosatha, kuti obzala ndi okolola akondwere pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Ngakhale tsopano amene akukolola akulandira malipiro ake, ndipo akututa mbewu ku moyo wosatha kuti wofesa ndi wokolola asangalale pamodzi. Onani mutuwo |