Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 4:37 - Buku Lopatulika

37 Pakuti m'menemo chonenacho chili choona, Wofesa ndi wina, womweta ndi winanso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Pakuti m'menemo chonenacho chili choona, Wofesa ndi wina, womweta ndi winanso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Paja amanenadi zoona aja amati, ‘Wobzala ndi wina, wokolola ndi winanso.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Nʼchifukwa chake mawu akuti, ‘Wina amafesa ndipo wina amakolola’ ndi woona.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 4:37
7 Mawu Ofanana  

Ndibzale ine nadye wina, ndi zondimerera ine zizulidwe.


Udzafesa koma osacheka; udzaponda azitona koma osadzola mafuta; udzaponda mphesa koma osamwa vinyo.


pakuti ndinakuopani, popeza inu ndinu munthu wouma mtima: munyamula chimene simunachiike pansi, mututa chimene simunachifese.


Indetu, indetu, ndinena kwa inu, Wokhulupirira Ine, ntchito zimene ndichita Ine adzazichitanso iyeyu; ndipo adzachita zoposa izi; chifukwa ndipita Ine kwa Atate.


Wakumweta alandira kulipira, nasonkhanitsira chobala kumoyo wosatha; kuti wofesayo akakondwere pamodzi ndi womwetayo.


Ine ndinatuma inu kukamweta chimene simunagwirirapo ntchito: ena anagwira ntchito, ndipo inu mwalowa ntchito yao.


Ndipo kunali, akabzala Israele, amakwera Amidiyani, ndi Amaleke, ndi ana a kum'mawa, inde amawakwerera;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa