Yohane 4:32 - Buku Lopatulika32 Koma Iye anati kwa iwo, Ine ndili nacho chakudya chimene inu simuchidziwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Koma Iye anati kwa iwo, Ine ndili nacho chakudya chimene inu simuchidziwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Koma Iye adati, “Ine ndili nacho chakudya chimene inu simukuchidziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Koma Iye anawawuza kuti, “Ine ndili ndi chakudya choti ndidye chimene inu simukuchidziwa.” Onani mutuwo |