Yohane 4:33 - Buku Lopatulika33 Chifukwa chake ophunzira ananena wina ndi mnzake, Kodi pali wina anamtengera Iye kanthu kakudya? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Chifukwa chake ophunzira ananena wina ndi mnzake, Kodi pali wina anamtengera Iye kanthu kakudya? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Pamenepo ophunzirawo adayamba kufunsana kuti, “Kodi kapena wina wadzaŵapatsa kale chakudya?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Ndipo ophunzira ake anafunsana wina ndi mnzake kuti, “Kodi alipo wina amene anamubweretsera Iye chakudya?” Onani mutuwo |