Yohane 4:30 - Buku Lopatulika30 Anatuluka iwo m'mzinda ndipo analinkudza kwa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Anatuluka iwo m'mudzi ndipo analinkudza kwa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Apo anthuwo adatuluka m'mudzimo kubwera kwa Yesu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Iwo anatuluka mʼmudziwo ndi kupita kumene kunali Iye. Onani mutuwo |