Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 4:29 - Buku Lopatulika

29 Tiyeni, mukaone munthu, amene anandiuza zinthu zilizonse ndinazichita: ameneyu sali Khristu nanga?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Tiyeni, mukaone munthu, amene anandiuza zinthu zilizonse ndinazichita: ameneyu sali Khristu nanga?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 “Tiyeni, mukaone munthu amene wandiwuza zonse zimene ine ndidachita. Kodi ameneyu sangakhale Mpulumutsi wolonjezedwa uja kapena?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 “Tiyeni mukaone munthu amene wandiwuza ine zilizonse zimene ndinazichita. Kodi ameneyu sangakhale Khristu?”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 4:29
12 Mawu Ofanana  

Ndipo makamu onse a anthu anazizwa, nanena, Uyu si mwana wa Davide kodi?


Mkazi ananena ndi Iye, Ndidziwa kuti Mesiya adza (wotchedwa Khristu): akadzadza Iyeyu, adzatiuza zonse.


Pamenepo mkazi anasiya mtsuko wake, namuka mumzinda, nanena ndi anthu,


Anatuluka iwo m'mzinda ndipo analinkudza kwa Iye.


Ndipo m'mzinda muja anthu Asamariya ambiri anamkhulupirira Iye chifukwa cha mau a mkazi, wochita umboniyo, kuti, Anandiuza ine zinthu zilizonse ndinazichita.


Ndipo taona amalankhula poyera, ndipo sanena kanthu kwa Iye. Kapena kodi akulu adziwa ndithu kuti ndiye Khristu ameneyo?


Koma ambiri a m'khamu la anthu anakhulupirira Iye; ndipo ananena, Pamene Khristu akadza kodi adzachita zizindikiro zambiri zoposa zimene adazichita ameneyo?


Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena, Idzani. Ndipo wakumva anene, Idzani. Ndipo wakumva ludzu adze; iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere.


Ndipo Samuele anayankha Saulo nati, Ine ndine mlauliyo. Kwera, batsogola kumsanje, pakuti mudzadya ndi ine lero; ndipo m'mawa ndidzakulola upite, ndi kukudziwitsa zonse zili mumtima mwako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa