Yohane 4:12 - Buku Lopatulika12 Kodi muli wamkulu ndi atate wathu Yakobo amene anatipatsa ife chitsimechi, namwamo iye yekha, ndi ana ake, ndi zoweta zake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Kodi muli wamkulu ndi atate wathu Yakobo amene anatipatsa ife chitsimechi, namwamo iye yekha, ndi ana ake, ndi zoweta zake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Yakobe, kholo lathu ndiye adatipatsa chitsimechi, chimene mwiniwakeyo ankamwapo pamodzi ndi ana ake, ndiponso zoŵeta zake. Kodi Inu mungapambane iyeyo?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kodi Inu ndinu wamkulu kuposa kholo lathu Yakobo, amene anatipatsa chitsimechi ndipo iye ankamwanso monga anachita ana ake ndi ziweto zake?” Onani mutuwo |